فرمت MP3 • بالاترین وضوح صدا
فرمت MP3 • مناسب اینترنت ضعیفتر
ترانه و شعر با صدای Eli Njuchi
I'ts Trex (Trex, Trex, Trex...)
Eya ndibwela Eya ndibwela Eya, eya, eya Musakaike kunyumba ndibwela
(ooh ndibwela, ey) ndibwela Nane mami ndakusowani Ndatsala pang'ono, pang'ono chabe Musakaike kunyumba ndibwela
Ooh-ooh! Eya ndibwela Eya ndibwela (oh-ah) Eya, eya, eya Musakaike kunyumba ndibwela
Mumandidzutsa mam'mawa Kwacha bwanji ku Joni ko? Mumadziwa ndikanama Nde mumachivumbulutsa chi pemphero Mumayimba phone daily Mumandipemphelera daily Mwati mwezi wa nyuwere Mwana wanga iwe ubwere
Ndikubwe- era, ndikubwera mama Sindidumphitsa holiday Ndikubwera mama Ndatsala pang'ono, pang'ono chabe Musakaike kunyumba ndibwela
Ooh-ooh! Eya ndibwela Eya ndibwela (oh-ah) Eya, eya, eya Musakaike kunyumba ndibwela
Ooh-ooh! Eya (ooh-ooh!) Ndibwela (ooh-ooh!) Eya (ooh-ooh!) Ndibwela (oh-ah) Ndatsala pang'ono, pang'ono chabe Musakaike kunyumba ndibwela
Mkamabwera mgulako ka chitenje Mami mudzatcheneko thukuta langa M'dzandiphikire limanda
دیگر آثار شنیدنی از Eli Njuchi